Thandizani Free Online Madrasah
Thandizo lanu ndi lofunika kwambiri
Thandizani ntchito yathuyi kuti tipereke maphunziro achisilamu mwa ulere kwa aliyense.
Cholinga cha Thandizo lanu
Server Maintenance
Kukonza ndi kusamalira server yathuContent Development
Kulemba ndi kukonza zinthu zatsopanoDevelopment Team
Kuthandizira anthu omwe amatipatsira mayankho a mafunso anuWebsite Improvements
Kukonza ndi kukuza websiteThandizani Online (PayChangu)
Sankhani ndalama zomwe mukufuna kuthandiza ndipo mutuluke ndalama zanu mwachangu
