Kodi ndi zoyenera kuti mwamuna apemphe chilolezo kwa mkazi wake pamene akufuna kukwatira mkazi wachiwiri?
Ine ndi mkazi amene ndavomera kukwatiwa kwa mwamuna amene ali ndi mkazi kale. Ndiye ndinamva kuti mitala imayambitsa matenda opatsirana pogonana. Kodi izizi ndi zoona?